Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Masalimo 135:12 - Buku Lopatulika

12 Ndipo anapereka dziko lao likhale cholowa, cholowa cha kwa Israele anthu ake.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

12 Ndipo anapereka dziko lao likhale chosiyira, chosiyira cha kwa Israele anthu ake.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

12 Adapereka dziko lao kuti likhale choloŵa, choloŵa cha Aisraele, anthu ake.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

12 ndipo anapereka dziko lawo ngati cholowa, cholowa cha anthu ake Aisraeli.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 135:12
7 Mawu Ofanana  

Ndipo anapirikitsa amitundu pamaso pao, nawagawira cholowa chao, ndi muyeso, nakhalitsa mafuko a Israele m'mahema mwao.


Ndipo mulandire dzikoli ndi kuchita maere monga mwa mabanja anu; cholowa chao chichulukire ochulukawo, cholowa chao chichepere ochepawo; kumene maere amgwera munthu, kumeneko nkwake; mulandire cholowa chanu monga mwa mafuko a makolo anu.


ndipo tinalanda dziko lao, ndi kulipereka likhale cholowa chao cha Arubeni, ndi Agadi, ndi hafu la fuko la Manase.


Motero Yoswa analanda dziko lonse monga mwa zonse Yehova adazinena kwa Mose; ndipo Yoswa analipereka kwa Israele, likhale cholowa chao, fuko lililonse gawo lake. Ndipo dziko linapumula nkhondo.


Ndipo awa ndi mafumu a dzikolo amene Yoswa ndi ana a Israele anawakantha tsidya lija la Yordani kumadzulo, kuyambira Baala-Gadi m'chigwa cha Lebanoni mpaka phiri la Halaki lokwera kunka ku Seiri; ndipo Yoswa analipereka kwa mafuko a Israele, likhale laolao, monga mwa magawo ao;


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa