Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Masalimo 135:10 - Buku Lopatulika

10 Ndiye amene anapanda amitundu ambiri, napha mafumu amphamvu;

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

10 Ndiye amene anapanda amitundu ambiri, napha mafumu amphamvu;

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

10 Ndiye amene adaononga mitundu yambiri ya anthu, ndi kupha mafumu amphamvu aja,

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

10 Iye anakantha mitundu yambiri ya anthu ndi kupha mafumu amphamvu:

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 135:10
4 Mawu Ofanana  

Ndipo Israele anamkantha ndi lupanga lakuthwa, nalanda dziko lake likhale laolao, kuyambira Arinoni kufikira Yaboki, kufikira ana a Amoni; popeza malire a ana a Amoni ndiwo olimba.


Ndipo anamkantha iye, ndi ana ake aamuna ndi anthu ake onse, kufikira sanatsale ndi mmodzi yense; nalanda dziko lake likhale laolao.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa