Masalimo 132:8 - Buku Lopatulika8 Ukani, Yehova, lowani ku mpumulo wanu; Inu ndi hema wa mphamvu yanu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20148 Ukani, Yehova, lowani ku mpumulo wanu; Inu ndi hema wa mphamvu yanu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa8 Dzambatukani, Inu Chauta, ndi kupita ku malo anu kumene mumakhala, Inuyo pamodzi ndi bokosi lachipangano lofanizira mphamvu zanu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero8 ‘Dzukani Yehova, ndipo bwerani ku malo anu opumulira, Inuyo ndi Bokosi la Chipangano limene limafanizira mphamvu zanu. Onani mutuwo |