Masalimo 131:1 - Buku Lopatulika1 Yehova, mtima wanga sunadzikuze ndi maso anga sanakwezeke; ndipo sindinatsate zazikulu, kapena zodabwitsa zondiposa. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20141 Yehova, mtima wanga sunadzikuze ndi maso anga sanakwezeke; ndipo sindinatsate zazikulu, kapena zodabwitsa zondiposa. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa1 Chauta, mtima wanga ndi wosadzikuza, maso anga ndi osanyada. Sinditengeka mtima ndi zinthu zapamwamba ndi zodabwitsa. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero1 Inu Yehova, mtima wanga siwodzikuza, maso anga siwonyada; sinditengeteka mtima ndi zinthu zapamwamba ndi zodabwitsa. Onani mutuwo |