Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Masalimo 124:2 - Buku Lopatulika

2 Akadapanda kukhala nafe Yehova, pakutiukira anthu:

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

2 Akadapanda kukhala nafe Yehova, pakutiukira anthu:

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

2 Chauta akadapanda kukhala pa mbali yathu, pamene anthu adatiwukira,

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

2 akanapanda kukhala mbali yathu Yehova, potiwukira anthuwo,

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 124:2
8 Mawu Ofanana  

Pakuti andizinga agalu, msonkhano wa oipa wanditsekereza; andiboola m'manja anga ndi m'mapazi anga.


Yehova! Ha! Achuluka nanga akundisautsa ine! Akundiukira ine ndi ambiri.


Ambiri amati kwa moyo wanga, alibe chipulumutso mwa Mulungu.


Woipa aunguza wolungama, nafuna kumupha.


Mwa Mulungu ndidzalemekeza mau ake, mwa Yehova ndidzalemekeza mau ake.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa