Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Masalimo 119:7 - Buku Lopatulika

7 Ndidzakuyamikani ndi mtima woongoka, pakuphunzira maweruzo anu olungama.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

7 Ndidzakuyamikani ndi mtima woongoka, pakuphunzira maweruzo anu olungama.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

7 Ndidzakutamandani ndikuchita zoyenera, ndikaphunzira malangizo anu olungama.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

7 Ndidzakutamandani ndi mtima wolungama, pamene ndikuphunzira malamulo anu olungama.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 119:7
16 Mawu Ofanana  

Inu ndinu wodala Yehova; ndiphunzitseni malemba anu.


Muchitire mtumiki wanu monga mwa chifundo chanu, ndipo ndiphunzitseni malemba anu.


Milomo yanga itulutse chilemekezo; popeza mundiphunzitsa malemba anu.


Mundizindikiritse njira ya malangizo anu; kuti ndilingalire zodabwitsa zanu.


Dziko lapansi lidzala nacho chifundo chanu, Yehova; mundiphunzitse malemba anu.


Manja anu anandilenga nandiumba; mundizindikiritse, kuti ndiphunzire malemba anu.


Mundiphunzitse chokonda Inu; popeza Inu ndinu Mulungu wanga; Mzimu wanu ndi wokoma; munditsogolere kuchidikha.


Ndidzayamika Yehova ndi mtima wanga wonse; ndidzawerengera zodabwitsa zanu zonse.


Atero Yehova, Mombolo wako, Woyera wa Israele, Ine ndine Yehova, Mulungu wako, amene ndikuphunzitsa kupindula, amene ndikutsogolera m'njira yoyenera iwe kupitamo.


Chalembedwa mwa aneneri, Ndipo adzakhala onse ophunzitsidwa ndi Mulungu. Yense amene adamva kwa Atate, naphunzira, adza kwa Ine.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa