Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Masalimo 119:6 - Buku Lopatulika

6 Pamenepo sindidzachita manyazi, pakupenyerera malamulo anu onse.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

6 Pamenepo sindidzachita manyazi, pakupenyerera malamulo anu onse.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

6 Tsono anthu sadzandichititsa manyazi, ndikatsata malamulo anu onse.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

6 Pamenepo ine sindikanachititsidwa manyazi, poganizira malamulo anu onse.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 119:6
10 Mawu Ofanana  

Pakuti pamenepo udzakondwera naye Wamphamvuyonse, ndi kuweramutsa nkhope yako kwa Mulungu.


Mundichirikize monga mwa mau anu, kuti ndikhale ndi moyo; ndipo ndisachite manyazi pa chiyembekezo changa.


Chifukwa chake ndiyesa ngolunjika malangizo anu onse akunena zonse; koma ndidana nazo njira zonse zonyenga.


Ndimamatika nazo mboni zanu; musandichititse manyazi, Yehova.


Mtima wanga ukhale wangwiro m'malemba anu; kuti ndisachite manyazi.


Muli abwenzi anga inu, ngati muzichita zimene ndikulamulani inu.


Pakuti aliyense amene angasunge malamulo onse, koma akakhumudwa pa limodzi, iyeyu wachimwira onse.


Ndipo tsopano, tiana, khalani mwa Iye; kuti akaonekere Iye tikakhale nako kulimbika mtima, osachita manyazi kwa Iye pa kudza kwake.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa