Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Masalimo 119:5 - Buku Lopatulika

5 Ha? Mwenzi zitakhazikika njira zanga kuti ndisamalire malemba anu.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

5 Ha? Mwenzi zitakhazikika njira zanga kuti ndisamalire malemba anu.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

5 Ndikadakonda kuti njira zanga zikhale zokhulupirika, pakumvera malamulo anu.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

5 Aa! Ndikanakonda njira zanga zikanakhala zokhazikika pa kumvera zophunzitsa zanu!

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 119:5
11 Mawu Ofanana  

Ndinatsegula pakamwa panga, ndi kupuma wefuwefu; popeza ndinakhumba malamulo anu.


Penyani kuti ndikonda malangizo anu; mundipatse moyo, Yehova, monga mwa chifundo chanu.


Dzanja lanu likhale lakundithandiza; popeza ndinasankha malangizo anu.


Ndidzathamangira njira ya malamulo anu, mutakulitsa mtima wanga.


Lingitsani mtima wanga kumboni zanu, si ku chisiriro ai.


Mundilengere mtima woyera, Mulungu; mukonze mzimu wokhazikika m'kati mwanga.


Koma ili ndi pangano limene ndidzapangana ndi nyumba ya Israele atapita masiku aja, ati Yehova; ndidzaika chilamulo changa m'kati mwao, ndipo m'mtima mwao ndidzachilemba; ndipo ndidzakhala Mulungu wao, nadzakhala iwo anthu anga;


Ndipo Ambuye atsogolere bwino mitima yanu ilowe m'chikondi cha mulungu ndi m'chipiriro cha Khristu.


akuyeseni inu opanda chilema m'chinthu chilichonse chabwino, kuti muchite chifuniro chake; ndi kuchita mwa ife chomkondweretsa pamaso pake, mwa Yesu Khristu; kwa Iyeyu ukhale ulemerero kunthawi za nthawi. Amen.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa