Masalimo 119:1 - Buku Lopatulika1 Odala angwiro m'mayendedwe ao, akuyenda m'chilamulo cha Yehova. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20141 Odala angwiro m'mayendedwe ao, akuyenda m'chilamulo cha Yehova. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa1 Ngodala amene moyo wao ulibe choŵadzudzulira, amene amayenda motsata malamulo a Chauta. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero1 Odala ndi amene moyo wawo ulibe cholakwa, amene amayenda monga mwa malamulo a Yehova. Onani mutuwo |