Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Masalimo 118:29 - Buku Lopatulika

29 Yamikani Yehova, pakuti Iye ndiye wabwino, pakuti chifundo chake nchosatha.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

29 Yamikani Yehova, pakuti Iye ndiye wabwino, pakuti chifundo chake nchosatha.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

29 Thokozani Chauta pakuti ngwabwino, ndipo chikondi chake chosasinthika nchamuyaya.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

29 Yamikani Yehova chifukwa ndi wabwino; pakuti chikondi chake chosasinthika ndi chosatha.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 118:29
5 Mawu Ofanana  

Ndipo anathirirana mang'ombe, kulemekeza ndi kuyamika Yehova, ndi kuti, Pakuti ndiye wabwino, pakuti chifundo chake nchosalekeza pa Israele. Nafuula anthu onse ndi chimfuu chachikulu, pomlemekeza Yehova; popeza adamanga maziko a nyumba ya Yehova.


Koma chifundo cha Yehova ndicho choyambira nthawi yosayamba kufikira nthawi yosatha kwa iwo akumuopa Iye, ndi chilungamo chake kufikira kwa ana a ana;


Yamikani Yehova; pakuti Iye ndiye wabwino; pakuti chifundo chake nchosatha.


Anene tsono iwo akuopa Yehova, kuti chifundo chake nchosatha.


Ndidzatchula zachifundo chake cha Yehova, ndi matamando a Yehova, monga mwa zonse zimene Yehova wapereka kwa ife; ndi ubwino wake waukulu kwa banja la Israele, umene Iye wapereka kwa iwo, monga mwa chifundo chake, ndi monga mwa ntchito zochuluka za chikondi chake.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa