Masalimo 118:25 - Buku Lopatulika25 Tikupemphani, Yehova, tipulumutseni tsopano; tikupemphani, Yehova, tipindulitseni tsopano. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201425 Tikupemphani, Yehova, tipulumutseni tsopano; tikupemphani, Yehova, tipindulitseni tsopano. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa25 Tipulumutseni, tikukupemphani Inu Chauta. Chauta, tikukupemphani kuti zinthu zitiyendere bwino. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero25 Inu Yehova, tipulumutseni; Yehova, tipambanitseni. Onani mutuwo |