Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Masalimo 117:1 - Buku Lopatulika

1 Lemekezani Yehova, amitundu onse; muimbireni, anthu onse.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

1 Lemekezani Yehova, amitundu onse; muimbireni, anthu onse.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

1 Tamandani Chauta, inu mitundu yonse ya anthu. Mlemekezeni kwambiri, inu anthu a m'maiko onse.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

1 Tamandani Yehova, inu anthu a mitundu yonse; mulemekezeni Iye, inu mitundu ya anthu.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 117:1
12 Mawu Ofanana  

Zonse zakupuma zilemekeze Yehova. Aleluya.


Fuulirani kwa Mulungu, dziko lonse lapansi.


Dziko lonse lapansi lidzakugwadirani, ndipo lidzakuimbirani; ndzaimbira dzina lanu.


Anthu akuyamikeni, Mulungu; anthu onse akuyamikeni.


Amitundu onse mudawalenga adzadza nadzagwada pamaso panu, Ambuye; nadzalemekeza dzina lanu.


Ndiponso, Tamandani Ambuye, inu a mitundu yonse; ndipo anthu onse amtamande.


Ndani adzakhala wosaopa ndi wosalemekeza dzina lanu Ambuye? Chifukwa Inu nokha muli woyera; chifukwa mitundu yonse idzadza nidzalambira pamaso panu, popeza zolungama zanu zidaonetsedwa.


Ndipo aimba nyimbo yatsopano, ndi kunena, Muyenera kulandira bukulo, ndi kumasula zizindikiro zake; chifukwa mwaphedwa, ndipo mwagulira Mulungu ndi mwazi wanu anthu a mafuko onse, ndi manenedwe onse, ndi mitundu yonse,


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa