Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Masalimo 116:4 - Buku Lopatulika

4 Pamenepo ndinaitana dzina la Yehova; ndikuti, Yehova ndikupemphani landitsani moyo wanga.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

4 Pamenepo ndinaitana dzina la Yehova; ndikuti, Yehova ndikupemphani landitsani moyo wanga.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

4 Tsono ndidapemphera potchula dzina la Chauta kuti, “Chauta ndikukupemphani, pulumutsani moyo wanga.”

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

4 Pamenepo ndinayitana dzina la Yehova: “Inu Yehova, pulumutseni!”

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 116:4
20 Mawu Ofanana  

M'mene ndinasautsika ndinaitanira pa Yehova; anandiyankha nandiika motakasuka Yehova.


M'kusauka kwanga ndinaitana Yehova, ndipo ndinakuwira Mulungu wanga; mau anga anawamva mu Kachisi mwake, ndipo mkuwo wanga wa pankhope pake unalowa m'makutu mwake.


Landitsani moyo wanga kulupanga; wokondedwa wanga kumphamvu ya galu,


Masautso a mtima wanga akula, munditulutse m'zondipsinja.


Munthu uyu wozunzika anafuula, ndipo Yehova anamumva, nampulumutsa m'masautso ake onse.


Ndipo undiitane tsiku la chisautso, ndidzakulanditsa, ndipo iwe udzandilemekeza.


Bwererani Yehova, landitsani moyo wanga; ndipulumutseni chifukwa cha kukoma mtima kwanu.


Pakuti muimfa m'mosakumbukira Inu; m'mandamo adzakuyamikani ndani?


Koma wamsonkhoyo alikuima patali sanafune kungakhale kukweza maso kumwamba, komatu anadziguguda pachifuwa pake nanena, Mulungu, mundichitire chifundo, ine wochimwa.


Ndipo Yesu yemwe ndi ophunzira ake anaitanidwa kuukwatiwo.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa