Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Masalimo 116:3 - Buku Lopatulika

3 Zingwe za imfa zinandizinga, ndi zowawa za manda zinandigwira: ndinapeza nsautso ndi chisoni.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

3 Zingwe za imfa zinandizinga, ndi zowawa za manda zinandigwira: ndinapeza nsautso ndi chisoni.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

3 Misampha ya imfa idandizinga, zoopsa za m'dziko la akufa zidandigwera. Ndidaona mavuto, nkugwidwa ndi nthumanzi.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

3 Zingwe za imfa zinandizinga, zoopsa za ku dziko la anthu akufa zinandigwera; ndinapeza mavuto ndi chisoni.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 116:3
9 Mawu Ofanana  

Ndapindika, ndawerama kwakukulu; ndimayenda woliralira tsiku lonse.


Ndipo pokhala Iye m'chipsinjo mtima anapemphera kolimba koposa ndithu: ndi thukuta lake linakhala ngati madontho aakulu a mwazi alinkugwa pansi.


Ameneyo, m'masiku a thupi lake anapereka mapemphero ndi mapembedzero pamodzi ndi kulira kwakukulu ndi misozi kwa Iye amene anakhoza kumpulumutsa Iye muimfa, ndipo anamveka popeza anaopa Mulungu,


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa