Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Masalimo 116:2 - Buku Lopatulika

2 Popeza amanditcherera khutu lake, chifukwa chake ndidzaitanira Iye masiku anga onse.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

2 Popeza amanditcherera khutu lake, chifukwa chake ndidzaitanira Iye masiku anga onse.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

2 Iye amatchera khutu kuti andimve, nchifukwa chake ndidzampempha nthaŵi zonse pamene ndili moyo.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

2 Pakuti ananditchera khutu, ndidzayitana Iye masiku onse a moyo wanga.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 116:2
13 Mawu Ofanana  

Kodi adzadzikondweretsa naye Wamphamvuyonse, ndi kuitana kwa Mulungu nthawi zonse?


Wodalitsika Yehova, Pakuti adamva mau a kupemba kwanga.


Munditcherere khutu lanu; ndipulumutseni msanga. Mundikhalire ine thanthwe lolimba, nyumba yamalinga yakundisunga.


Pakuti Inu ndinu thanthwe langa ndi linga langa; ndipo chifukwa cha dzina lanu ndiyendetseni bwino, ndipo nditsogolereni.


Kuyembekeza ndayembekeza Yehova; ndipo anandilola, namva kufuula kwanga.


Yehova, Mulungu wa chipulumutso changa, ndinafuula pamaso panu usana ndi usiku.


Pakuti munandiponya mwakuya m'kati mwa nyanja, ndipo madzi anandizinga; mafunde anu onse a nyondonyondo anandimiza.


Ndipo anawanenera fanizo lakuti ayenera iwo kupemphera nthawi zonse, osafooka mtima;


Musadere nkhawa konse; komatu m'zonse ndi pemphero, ndi pembedzero, pamodzi ndi chiyamiko, zopempha zanu zidziwike kwa Mulungu.


Chitani khama m'kupemphera, nimudikire momwemo ndi chiyamiko;


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa