Masalimo 112:1 - Buku Lopatulika1 Aleluya. Wodala munthu wakuopa Yehova, wakukondwera kwambiri ndi malamulo ake. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20141 Aleluya. Wodala munthu wakuopa Yehova, wakukondwera kwambiri ndi malamulo ake. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa1 Tamandani Chauta! Ngwodala munthu woopa Chauta, wokonda kusunga malamulo ake. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero1 Tamandani Yehova. Wodala munthu amene amaopa Yehova, amene amakondwera kwambiri ndi malamulo ake. Onani mutuwo |