Masalimo 109:8 - Buku Lopatulika8 Masiku ake akhale owerengeka; wina alandire udindo wake. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20148 Masiku ake akhale owerengeka; wina alandire udindo wake. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa8 Masiku ake akhale oŵerengeka, wina alandire udindo wake. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero8 Masiku ake akhale owerengeka; munthu wina atenge malo ake a utsogoleri. Onani mutuwo |