Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Masalimo 109:9 - Buku Lopatulika

9 Ana ake akhale amasiye, ndi mkazi wake wamasiye.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

9 Ana ake akhale amasiye, ndi mkazi wake wamasiye.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

9 Ana ake akhale amasiye, ndipo mkazi wake akhale mfedwa.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

9 Ana ake akhale amasiye ndipo mkazi wake akhale wopanda mwamuna.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 109:9
3 Mawu Ofanana  

ndi mkwiyo wanga udzayaka, ndipo ndidzapha inu ndi lupanga; ndipo akazi anu adzakhala amasiye, ndi ana anu omwe.


Chifukwa chake mupereke ana ao kunjala, mupereke iwo kumphamvu ya lupanga; akazi ao akhale opanda ana, ndi amasiye; amuna ao aphedwe ndi imfa, ndi anyamata ao apandidwe ndi lupanga kunkhondo.


Ndife amasiye opanda atate, amai athu akunga akazi amasiye.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa