Masalimo 109:30 - Buku Lopatulika30 Ndidzayamika Yehova kwakukulu pakamwa panga; ndi pakati pa anthu aunyinji ndidzamlemekeza. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201430 Ndidzayamika Yehova kwakukulu pakamwa panga; ndi pakati pa anthu aunyinji ndidzamlemekeza. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa30 Ndidzathokoza Chauta kwambiri polankhula. Ndidzamtamanda pakati pa gulu la anthu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero30 Ndi pakamwa panga ndidzathokoza Yehova kwambiri; ndidzamutamanda mʼgulu lalikulu la anthu. Onani mutuwo |