Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Masalimo 109:29 - Buku Lopatulika

29 Otsutsana nane avale manyazi, nadzikute nacho chisokonezo chao ngati ndi chofunda.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

29 Otsutsana nane avale manyazi, nadzikute nacho chisokonezo chao ngati ndi chofunda.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

29 Ondineneza akhale onyozeka, manyazi ao aŵakute ngati chovala.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

29 Onditsutsa adzavekedwa mnyozo, ndipo adzadzifunditsa manyazi ngati chovala.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 109:29
9 Mawu Ofanana  

Iwo akudana nawe adzavala manyazi; ndi hema wa oipa adzakhala kuli zii.


Ndidzawaveka adani ake ndi manyazi; koma pa iyeyu korona wake adzamveka.


Kunena za mutu wao wa iwo akundizinga, choipa cha milomo yao chiwaphimbe.


Achite manyazi, nadodome iwo akukondwera chifukwa cha choipa chidandigwera. Avekeke ndi manyazi ndi kupunzika iwo akudzikuza pa ine.


Adzachita manyazi, nadzanthunthumira kwakukulu adani anga onse; adzabwerera, nadzachita manyazi modzidzimuka.


Koma Yehova ali ndi ine ngati wamphamvu ndi woopsa; chifukwa chake ondisautsa adzaphunthwa, sadzandilala; adzakhala ndi manyazi ambiri, chifukwa sanachite chanzeru, ngakhale ndi kunyazitsa kwamuyaya kumene sikudzaiwalika.


Ndipo ambiri a iwo ogona m'fumbi lapansi adzauka, ena kunka kumoyo wosatha, ndi ena kumanyazi ndi mnyozo wosatha.


Pamenepo mdani wanga adzachiona, ndi manyazi adzamkuta iye amene adati kwa ine, Ali kuti Yehova Mulungu wako? Maso anga adzamuona; tsopano adzampondereza ngati thope la m'miseu.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa