Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Masalimo 109:3 - Buku Lopatulika

3 Ndipo anandizinga ndi mau a udani, nalimbana nane kopanda chifukwa.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

3 Ndipo anandizinga ndi mau a udani, nalimbana nane kopanda chifukwa.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

3 Ponseponse amandilankhula mau achidani, amandinena popanda chifukwa.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

3 Andizungulira ndi mawu audani, amandinena popanda chifukwa.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 109:3
14 Mawu Ofanana  

Ndipo Abisalomu anaitana Ahitofele Mgiloni, phungu wa Davide, kumzinda wake ndiwo Gilo, pamene iye analikupereka nsembe. Ndipo chiwembucho chinali cholimba; pakuti anthu anachulukachulukabe kwa Abisalomu.


Tsopano anatizinga m'mayendedwe athu, apenyetsetsa m'maso kuti atigwetse pansi.


Ng'ombe zamphongo zambiri zandizinga; mphongo zolimba za ku Basani zandizungulira.


Adani anga asandikondwerere ine monyenga; okwiya nane kopanda chifukwa asanditsinzinire.


Pakuti salankhula zamtendere, koma apangira chiwembu odekha m'dziko.


Pakuti ananditchera ukonde wao m'mbunamo kopanda chifukwa, anakumbira moyo wanga dzenje kopanda chifukwa.


Ondida kopanda chifukwa achuluka koposa tsitsi la pamutu panga; ofuna kunditha, ndiwo adani anga monama, ali ndi mphamvu. Pamenepo andibwezetsa chosafunkha ine.


Zinandizungulira ngati madzi tsiku lonse; zinandizinga pamodzi.


Efuremu andizinga ndi bodza, ndi nyumba ya Israele ndi chinyengo, ndi Yuda apikisana ndi Mulungu, ndiye Woyera wokhulupirika.


Nati iye, Chifukwa ninji mbuye wanga amalondola mnyamata wake? Pakuti ndachitanji? Kapena m'dzanja langa muli choipa chotani?


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa