Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Masalimo 109:2 - Buku Lopatulika

2 pakuti pakamwa pa woipa ndi pakamwa pa chinyengo pananditsegukira; anandilankhulira ndi m'kamwa mwa bodza.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

2 pakuti pakamwa pa woipa ndi pakamwa pa chinyengo pananditsegukira; anandilankhulira ndi m'kamwa mwa bodza.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

2 pakuti anthu oipa ndi onama amakamba zondiwukira, amalankhula zondinamizira.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

2 pakuti anthu oyipa ndi achinyengo atsekula pakamwa pawo kutsutsana nane; iwo ayankhula motsutsana nane ndi malilime abodza.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 109:2
16 Mawu Ofanana  

chifukwa kuti ndinabedwa ndithu m'dziko la Ahebri; ndiponso pano sindinachite kanthu kakundiikira ine m'dzenjemu.


Ndipo Ahitofele ananena ndi Abisalomu, Ndiloleni ndisankhe tsopano anthu zikwi khumi ndi ziwiri, ndipo ndidzanyamuka usiku womwe uno ndi kulondola Davide;


Anola lilime lao ngati njoka; pansi pa milomo yao pali ululu wa mphiri.


Pakuti ndamva ugogodi wa ambiri, mantha andizinga. Pondipangira chiwembu, anatsimikiza mtima kulanda moyo wanga.


Ikhale yosalankhula milomo ya mabodza, imene imalankhula mwachipongwe pa olungama mtima, ndi kudzikuza ndi kunyoza.


ukonda mau onse akuononga, lilime lachinyengo, iwe.


Mlomo wa ntheradi ukhazikika nthawi zonse; koma lilime lonama likhala kamphindi.


Mtima wa wolungama uganizira za mayankhidwe; koma m'kamwa mwa ochimwa mutsanulira zoipa.


Maso akunyada, lilime lonama, ndi manja akupha anthu osachimwa;


Ndipo apinda lilime lao ngati uta wao, liname; koma akula mphamvu m'dzikomo, koma si pachoonadi; pakuti alinkunkabe nachita zoipa, ndipo sandidziwa Ine, ati Yehova.


Ndipo yense adzanyenga mnansi wake, osanena choonadi; aphunzitsa lilime lao kunena zonama; nadzithodwetsa kuchita zoipa.


naimika mboni zonama, zakunena, Munthu ameneyo saleka kunenera malo oyera amene, ndi chilamulo;


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa