Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Masalimo 109:26 - Buku Lopatulika

26 Ndithandizeni Yehova, Mulungu wanga: Ndipulumutseni monga mwa chifundo chanu;

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

26 Ndithandizeni Yehova, Mulungu wanga: Ndipulumutseni monga mwa chifundo chanu;

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

26 Thandizeni Chauta, Mulungu wanga. Pulumutseni chifukwa cha chikondi chanu chosasinthika.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

26 Thandizeni Inu Yehova Mulungu wanga; pulumutseni molingana ndi chikondi chanu.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 109:26
6 Mawu Ofanana  

Malamulo anu onse ngokhulupirika; andilondola nalo bodza; ndithandizeni.


Pakuti zoipa zosawerengeka zandizinga, zochimwa zanga zandipeza kotero kuti sindikhoza kupenya; ziposa tsitsi la mutu wanga, ndipo wandichokera mtima.


Mundichitire chifundo, Mulungu, mundichitire chifundo; pakuti moyo wanga ukhulupirira Inu, ndipo ndithawira kumthunzi wa mapiko anu, kufikira zosakazazo zidzapita.


Koma ine, pemphero langa lili kwa Inu, Yehova, m'nyengo yolandirika; Mulungu, mwa chifundo chanu chachikulu, mundivomereze ndi choonadi cha chipulumutso chanu.


Mundiyankhe Yehova; pakuti chifundo chanu nchokoma; munditembenukire monga mwa unyinji wa nsoni zokoma zanu.


Ameneyo, m'masiku a thupi lake anapereka mapemphero ndi mapembedzero pamodzi ndi kulira kwakukulu ndi misozi kwa Iye amene anakhoza kumpulumutsa Iye muimfa, ndipo anamveka popeza anaopa Mulungu,


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa