Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Masalimo 109:25 - Buku Lopatulika

25 Ndiwakhaliranso chotonza; pakundiona apukusa mutu.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

25 Ndiwakhaliranso chotonza; pakundiona apukusa mutu.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

25 Ondineneza amandinyodola, akandiwona amapukusa mitu yao.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

25 Ndine chinthu chotonzedwa kwa otsutsana nane; akandiona, amapukusa mitu yawo.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 109:25
13 Mawu Ofanana  

Inenso ndikadanena monga inu, moyo wanu ukadakhala m'malo mwa moyo wanga, ndikadalumikizanitsa mau akutsutsana nanu, ndi kukupukusirani mutu wanga.


Adadzitengera kwa Yehova; kuti adzampulumutsa, amlanditse tsopano popeza akondwera naye.


awa ndiwo mau amene Yehova wanena za iye, Namwali, mwana wamkazi wa Ziyoni, wakunyoza iwe ndi kuseka iwe ndi chiphwete; mwana wamkazi wa Yerusalemu wapukusa mutu wake pambuyo pako.


Ndipo iwo akupitirirapo anamchitira mwano, napukusa mitu yao, nanena, Ha! Iwe wakupasula Kachisi, ndi kummanga masiku atatu,


Pakuti Khristunso sanadzikondweretse yekha; koma monga kwalembedwa, Minyozo ya iwo amene anakunyoza iwe inagwa pa Ine.


Yesu, ameneyo, chifukwa cha chimwemwe choikidwacho pamaso pake, anapirira mtanda, nanyoza manyazi, nakhala padzanja lamanja la mpando wachifumu wa Mulungu.


Chifukwa chake titulukire kwa Iye kunja kwa tsasa osenza tonzo lake.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa