Masalimo 109:22 - Buku Lopatulika22 Pakuti ine ndine wozunzika ndi waumphawi, ndi mtima wanga walaswa m'kati mwanga. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201422 Pakuti ine ndine wozunzika ndi waumphawi, ndi mtima wanga walaswa m'kati mwanga. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa22 Pakuti ine ndine wosauka ndi wosoŵa, ndipo mtima wanga ukuŵaŵa kwambiri. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero22 Pakuti ndine wosauka ndi wosowa, ndipo mtima wanga ukuwawa mʼkati mwanga. Onani mutuwo |