Masalimo 109:21 - Buku Lopatulika21 Koma Inu, Yehova Ambuye, muchite nane chifukwa cha dzina lanu; ndilanditseni popeza chifundo chanu ndi chabwino. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201421 Koma Inu, Yehova Ambuye, muchite nane chifukwa cha dzina lanu; ndilanditseni popeza chifundo chanu ndi chabwino. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa21 Koma Inu Mulungu, Ambuye anga, munditchinjirize malinga ndi ulemerero wa dzina lanu, mundipulumutse chifukwa chikondi chanu chosasinthika ndi chabwino. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero21 Koma Inu Ambuye Wamphamvuzonse, muchite nane molingana ndi dzina lanu, chifukwa cha ubwino wa chikondi chanu, pulumutseni. Onani mutuwo |