Masalimo 109:19 - Buku Lopatulika19 Limkhalire ngati chovala adzikuta nacho, ndi lamba limene adzimangirira nalo m'chuuno chimangirire. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201419 Limkhalire ngati chovala adzikuta nacho, ndi lamba limene adzimangirira nalo m'chuuno chimangirire. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa19 Matemberero akhale ngati mwinjiro wofundira, ngati lamba wovala tsiku ndi tsiku. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero19 Matemberero akhale ngati chofunda chodzikutira nacho, ngati lamba wovala tsiku ndi tsiku. Onani mutuwo |