Masalimo 109:18 - Buku Lopatulika18 Anavalanso temberero ngati malaya, ndipo lidamlowa m'kati mwake ngati madzi, ndi ngati mafuta m'mafupa ake. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201418 Anavalanso temberero ngati malaya, ndipo lidamlowa m'kati mwake ngati madzi, ndi ngati mafuta m'mafupa ake. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa18 Kutemberera anzake kunali ngati chovala chake, motero matemberero amgwere ngati mvula. Akhale ngati mafuta oloŵa m'mafupa mwake. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero18 Anavala kutemberera ngati chovala; kutemberera kunalowa mʼthupi lake ngati madzi, kulowa mʼmafupa ake ngati mafuta. Onani mutuwo |