Masalimo 109:11 - Buku Lopatulika11 Wokongoletsa agwire zonse ali nazo; ndi alendo alande za ntchito yake. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201411 Wokongoletsa agwire zonse ali nazo; ndi alendo alande za ntchito yake. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa11 Wokongoza ndalama amlande zonse zimene ali nazo. Alendo afunkhe zimene adapindula ndi ntchito yake. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero11 Wokongoza alande zonse zimene ali nazo; alendo afunkhe ntchito za manja ake. Onani mutuwo |