Masalimo 104:9 - Buku Lopatulika9 Munaika malire kuti asapitirireko; kuti asabwererenso kuphimba dziko lapansi. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20149 Munaika malire kuti asapitirireko; kuti asabwererenso kuphimba dziko lapansi. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa9 Madziwo Inu mudaŵaikira malire oti asabzole, kuti asaphimbenso dziko lapansi. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero9 Inu munayika malire ndipo sangathe kudutsa, iwo sadzamizanso dziko lapansi. Onani mutuwo |