Masalimo 104:10 - Buku Lopatulika10 Atumiza akasupe alowe m'makwawa; ayenda pakati pa mapiri: Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201410 Atumiza akasupe alowe m'makwawa; ayenda pakati pa mapiri: Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa10 Inu mumatumphutsa akasupe m'zigwa, mitsinje imayenda pakati pa mapiri. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero10 Iye achititsa akasupe kutulutsa madzi kupita ku zigwa; madziwo amayenda pakati pa mapiri. Onani mutuwo |