Masalimo 104:8 - Buku Lopatulika8 anakwera m'mapiri, anatsikira m'zigwa, kufikira malo mudawakonzeratu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20148 anakwera m'mapiri, anatsikira m'zigwa, kufikira malo mudawakonzeratu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa8 Mapiri adatumphuka, zigwa zidatsika, mpaka kumene Inu mudaakonzeratu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero8 Inu munamiza mapiri, iwo anatsikira ku zigwa kumalo kumene munawakonzera. Onani mutuwo |