Masalimo 104:7 - Buku Lopatulika7 Pa kudzudzula kwanu anathawa; anathawa msanga liu la bingu lanu; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20147 Pa kudzudzula kwanu anathawa; anathawa msanga liu la bingu lanu; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa7 Mutaŵadzudzula, madziwo adathaŵa, atamva mkokomo wa bingu lanu, adamwazika. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero7 Koma pakudzudzula kwanu madzi anathawa, pa mkokomo wa bingu lanu iwo anamwazika; Onani mutuwo |