Masalimo 104:6 - Buku Lopatulika6 Mudalikuta ndi nyanja ngati ndi chovala; madzi anafikira pamwamba pa mapiri. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20146 Mudalikuta ndi nyanja ngati ndi chovala; madzi anafikira pamwamba pa mapiri. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa6 Mudaliphimba ndi nyanja yozama ngati ndi chovala, ndipo madzi adakwera mpaka pamwamba pa mapiri. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero6 Munaliphimba ndi nyanja yozama ngati chovala; madzi anayimirira pamwamba pa mapiri. Onani mutuwo |