Masalimo 104:2 - Buku Lopatulika2 muvala ulemu ndi chifumu. Amene mudzikuta nako kuunika monga ndi chovala; ndi kuyala thambo ngati nsalu yotchinga. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20142 muvala ulemu ndi chifumu. Amene mudzikuta nako kuunika monga ndi chovala; ndi kuyala thambo ngati nsalu yotchinga. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa2 Mumadzifunditsa ndi kuŵala ngati chovala, mwatambasula mlengalenga ngati hema. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero2 Iye wadzifunditsa kuwala ngati chovala; watambasula miyamba ngati tenti Onani mutuwo |