Masalimo 104:1 - Buku Lopatulika1 Lemekeza Yehova, moyo wanga; Yehova, Mulungu wanga, Inu ndinu wamkulukulu; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20141 Lemekeza Yehova, moyo wanga; Yehova, Mulungu wanga, Inu ndinu wamkulukulu; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa1 Tamanda Chauta, iwe mtima wanga. Inu Chauta, Mulungu wanga, ndinu aakulu kwambiri. Mumavala ulemu ndi ufumu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero1 Tamanda Yehova, iwe moyo wanga. Inu Yehova Mulungu wanga, ndinu wamkulu kwambiri; mwavala ulemerero ndi ufumu. Onani mutuwo |