Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Masalimo 104:12 - Buku Lopatulika

12 Mbalame za mlengalenga zifatsa pamenepo, zimaimba pakati pa mitawi.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

12 Mbalame za mlengalenga zifatsa pamenepo, zimaimba pakati pa mitawi.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

12 Mbalame zimamanga zisa pafupi ndi mitsinjeyo, zimaimba m'nthambi za mitengo.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

12 Mbalame zamlengalenga zimayika zisa mʼmbali mwa madzi; zimayimba pakati pa thambo.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 104:12
7 Mawu Ofanana  

Amene apatsa zoweta chakudya chao, ana a khwangwala alikulira.


Nyama zakuthengo ndi zoweta zonse; zokwawa, ndi mbalame zakuuluka.


Ndidziwa mbalame zonse za m'mapiri, ndipo nyama zakuthengo zili ndi Ine.


Mbawanso inapeza nyumba, ndi namzeze chisa chake choikamo ana ake, pa maguwa a nsembe anu, Yehova wa makamu, mfumu yanga ndi Mulungu wanga.


Yang'anirani mbalame za kumwamba, kuti sizimafesa ai, kapena sizimatema ai, kapena sizimatutira m'nkhokwe; ndipo Atate wanu wa Kumwamba azidyetsa. Nanga inu mulibe kusiyana nazo kuziposa kodi?


Ndipo Yesu ananena kwa iye, Ankhandwe ali nazo nkhwimba zao, ndi mbalame za m'mlengalenga zisa zao, koma Mwana wa Munthu alibe potsamira mutu wake.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa