Masalimo 104:11 - Buku Lopatulika11 Zimamwamo nyama zonse zakuthengo; mbidzi zipherako ludzu lao. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201411 Zimamwamo nyama zonse za kuthengo; mbidzi zipherako ludzu lao. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa11 Imapatsa nyama zonse zakuthengo madzi akumwa, mbidzi zimapherapo ludzu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero11 Iwo amapereka madzi kwa zirombo zonse zakuthengo; abulu akuthengo amapha ludzu lawo. Onani mutuwo |