Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Masalimo 103:9 - Buku Lopatulika

9 Sadzatsutsana nao nthawi zonse; ndipo sadzasunga mkwiyo wake kosatha.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

9 Sadzatsutsana nao nthawi zonse; ndipo sadzasunga mkwiyo wake kosatha.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

9 Akatikalipira, mkwiyo wake sudzakhala woyaka mpakampaka.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

9 Iye sadzatsutsa nthawi zonse, kapena kusunga mkwiyo wake kwamuyaya;

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 103:9
7 Mawu Ofanana  

Pakuti mkwiyo wake ukhala kanthawi kokha; koma kuyanja kwake moyo wonse. Kulira kuchezera, koma mamawa kuli kufuula kokondwera.


Munalimbana naye pang'ono, pamene munamchotsa; wamchotsa iye kuomba kwake kolimba tsiku la mphepo yamlumbanyanja.


Pakuti sindidzatsutsana kunthawi zonse, sindidzakwiya masiku onse; pakuti mzimu udzalefuka pamaso pa Ine, ndi miyoyo imene ndinailenga.


Pita; nulalikire mau awa kuyang'ana kumpoto, ndi kuti, Bwera iwe Israele wobwerera, ati Yehova; sindidzakuyang'anira iwe ndi kukwiya; pakuti Ine ndili wachifundo, ati Yehova, sindidzakhala nako kukwiya kunthawi zonse.


Kodi adzasunga mkwiyo wake kunthawi zonse? Kodi adzakudikira mpaka chimaliziro? Taona, wanena ndi kuchita zoipa monga unatero.


Zoipa zake zilizonse anazichita sizidzakumbukika zimtsutse, anachita choyenera ndi cholungama, adzakhala ndi moyo ndithu.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa