Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Masalimo 103:10 - Buku Lopatulika

10 Sanatichitira monga mwa zolakwa zathu, kapena kutibwezera monga mwa mphulupulu zathu.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

10 Sanatichitira monga mwa zolakwa zathu, kapena kutibwezera monga mwa mphulupulu zathu.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

10 Satilanga moyenerera machimo athu, satibwezera molingana ndi zolakwa zathu.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

10 satichitira molingana ndi machimo athu, kapena kutibwezera molingana ndi mphulupulu zathu.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 103:10
8 Mawu Ofanana  

Ndipo zitatigwera zonsezi chifukwa cha ntchito zathu zoipa ndi kupalamula kwathu kwakukulu; popeza inu Mulungu wathu mwatilanga motichepsera mphulupulu zathu, ndi kutipatsa chipulumutso chotere;


Ndipo mwa nsoni zanu zochuluka simunawathe, kapena kuwataya; popeza Inu ndinu Mulungu wa chisomo ndi chifundo.


nakufotokozere zinsinsi za nzeru, popeza zipindikapindika machitidwe ao! Chifukwa chake dziwa kuti Mulungu akuiwalira mphulupulu zina.


Apenyerera anthu, ndi kuti, ndinachimwa, ndaipsa choongokacho, ndipo sindinapindule nako.


Mukasunga mphulupulu, Yehova, adzakhala chilili ndani, Ambuye?


Chifukwa chakusathedwa ife ndicho chifundo cha Yehova, pakuti chisoni chake sichileka,


Yehova, ndinamva mbiri yanu ndi mantha; Yehova, tsitsimutsani ntchito yanu pakati pa zaka, pakati pa zaka mudziwitse; pa mkwiyo mukumbukire chifundo.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa