Masalimo 103:11 - Buku Lopatulika11 Pakuti monga m'mwamba mutalikira ndi dziko lapansi, motero chifundo chake chikulira iwo akumuopa Iye. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201411 Pakuti monga m'mwamba mutalikira ndi dziko lapansi, motero chifundo chake chikulira iwo akumuopa Iye. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa11 Monga kumwamba kuli kutali ndi dziko lapansi, ndi momwenso chidakulira chikondi chake chosasinthika kwa anthu oopa Chauta. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero11 Pakuti monga kumwamba kuli kutali ndi dziko lapansi, koteronso chikondi chake nʼchachikulu kwa iwo amene amamuopa; Onani mutuwo |