Masalimo 103:2 - Buku Lopatulika2 Lemekeza Yehova, moyo wanga, ndi kusaiwala zokoma zake zonse atichitirazi: Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20142 Lemekeza Yehova, moyo wanga, ndi kusaiwala zokoma zake zonse atichitirazi: Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa2 Tamanda Chauta, iwe mtima wanga, ndipo usaiŵale zabwino zake zonse. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero2 Tamanda Yehova, iwe moyo wanga, ndipo usayiwale zabwino zake zonse. Onani mutuwo |