Masalimo 103:1 - Buku Lopatulika1 Lemekeza Yehova, moyo wanga; ndi zonse za m'kati mwanga zilemekeze dzina lake loyera. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20141 Lemekeza Yehova, moyo wanga; ndi zonse za m'kati mwanga zilemekeze dzina lake loyera. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa1 Tamanda Chauta, iwe mtima wanga, moyo wanga wonse umuyamike potchula dzina lake loyera. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero1 Tamanda Yehova, iwe moyo wanga; ndi zonse zamʼkati mwanga zitamande dzina lake loyera. Onani mutuwo |