Masalimo 103:16 - Buku Lopatulika16 Pakuti mphepo ikapitapo pakhala palibe: Ndi malo ake salidziwanso. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201416 Pakuti mphepo ikapitapo pakhala palibe: Ndi malo ake salidziwanso. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa16 Koma mphepo ikaombapo, duŵalo pamakhala palibe, siliwonekanso pa malo ake. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero16 koma mphepo imawombapo ndipo silionekanso ndipo malo ake sakumbukirikanso. Onani mutuwo |