Masalimo 102:12 - Buku Lopatulika12 Koma Inu, Yehova, mukhalabe kunthawi yonse; ndi chikumbukiro chanu ku mibadwomibadwo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201412 Koma Inu, Yehova, mukhalabe kunthawi yonse; ndi chikumbukiro chanu ku mibadwomibadwo. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa12 Koma Inu Chauta, mumakhala pa mpando wanu waufumu mpaka muyaya. Anthu a mibadwo yonse adzakukumbukirani. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero12 Koma Inu Yehova, muli pa mpando wanu waufumu kwamuyaya; kudziwika kwanu ndi kokhazikika ku mibado yonse. Onani mutuwo |