Masalimo 100:2 - Buku Lopatulika2 Tumikirani Yehova ndi chikondwerero: Idzani pamaso pake ndi kumuimbira mokondwera. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20142 Tumikirani Yehova ndi chikondwerero: Idzani pamaso pake ndi kumuimbira mokondwera. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa2 Tumikirani Chauta mosangalala. Bwerani pamaso pake mukuimba mokondwa. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero2 Mulambireni Yehova mosangalala; bwerani pamaso pake ndi nyimbo zachikondwerero. Onani mutuwo |
Ndipo mukondwere pamaso pa Yehova Mulungu wanu, inu ndi ana anu aamuna, ndi ana anu aakazi, ndi antchito anu aamuna, ndi antchito anu aakazi, ndi Mlevi wokhala m'mudzi mwanu, ndi mlendo, ndi mwana wamasiye, ndi mkazi wamasiye, okhala pakati pa inu, m'malo amene Yehova Mulungu wanu adzasankha kukhalitsako dzina lake.