Masalimo 10:6 - Buku Lopatulika6 Ati mumtima mwake, Sindidzagwedezeka ine; ku mibadwomibadwo osagwa m'tsoka ine. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20146 Ati mumtima mwake, Sindidzagwedezeka ine; ku mibadwomibadwo osagwa m'tsoka ine. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa6 Mumtima mwake amaganiza kuti, “Sindidzagwedezeka, sindidzaona konse mavuto.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero6 Iye amadziyankhulira kuti, “Palibe chimene chidzandigwedeze. Ndidzakhala wokondwa nthawi zonse ndipo sindidzakhala pa mavuto.” Onani mutuwo |