Masalimo 10:5 - Buku Lopatulika5 Mayendedwe ake alimbika nthawi zonse; maweruzo anu ali pamwamba posaona iye; adani ake onse awanyodola. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20145 Mayendedwe ake alimbika nthawi zonse; maweruzo anu ali pamwamba posaona iye; adani ake onse awanyodola. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa5 Zinthu zimamuyendera bwino nthaŵi zonse. Chiweruzo chanu chili naye kutali, ndipo salabadako konse. Kunena za adani ake, iye amangoŵanyodola. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero5 Zinthu zake zimamuyendera bwino; iye ndi wamwano ndipo malamulo anu ali nawo kutali; amanyogodola adani ake onse. Onani mutuwo |