Marko 9:11 - Buku Lopatulika11 Ndipo anamfunsa Iye, nanena, Nanga alembi anena kuti adzayamba kufika Eliya? Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201411 Ndipo anamfunsa Iye, nanena, Nanga alembi anena kuti adzayamba kufika Eliya? Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa11 Tsono adamufunsa kuti, “Nanga bwanji aphunzitsi a Malamulo amati Eliya adzayenera kuyamba wabwera?” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero11 Ndipo anamufunsa Iye kuti, “Nʼchifukwa chiyani aphunzitsi amalamulo amati Eliya ayenera kuyamba wabwera?” Onani mutuwo |