Marko 8:9 - Buku Lopatulika9 Ndipo iwo anali ngati zikwi zinai; ndipo Iye analawirana nao. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20149 Ndipo iwo anali ngati zikwi zinai; ndipo Iye analawirana nao. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa9 Anthu amene adaali pamenepo, amuna okha adaalipo ngati zikwi zinai. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero9 Panali amuna pafupifupi 4,000. Ndipo atawawuza kuti apite kwawo, Onani mutuwo |